MWAMBO OGAWA NNGONGOLE YA ZIPANGIZO ZA ULIMI UKUPITILIRA KU RUMPHI
Jan 29, 2025
Wachiwiri kwa nduna ya zamalimidwe Olemekezeka a Benedicto Chambo komanso Paramount Chief Themba la maThemba Chikulamayembe motsogozedwa ndi nkulu wa bungwe la NEEF, a Humphrey Mdyetseni kukhazikitsa mwambo opeleka feteleza wa ngongole ya ulimi m'boma la Rumphi.